Skip to content

Precious Katema

Organisation MIJFM

Country Malawi

Region Southern Africa

Sector

Position/Job title Reporter

map

My experience in adult learning and education

Ndine okopeka maka kuchita nawo maphunziro omwe akonzedwa chifukwa zindithandizira pakalembedwe kanga ka nkhani maka zokhunza maphunziro anthu akuluakulu podzindikiranso mavuto omwe amakumana nawo nthawi yophunzira komanso powululira kufunika kwamaphunzirowa. Chinthu china zindithandizira kuwonjezera ukadaulo omwe inali pakalembedwe ka nkhani zomwe zimakhuza maphunziro akuluakulu muno M'malawi.